Deuteronomo 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Usalephere kupereka chakhumi cha mbewu zako zonse zokolola m’munda mwako chaka ndi chaka.+