Levitiko 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uzani ana a Isiraeli kuti, ‘Zolengedwa zimene mungadye+ pa nyama zonse zimene zili padziko lapansi ndi izi: Deuteronomo 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitundu ya nyama zimene muyenera kudya ndi izi:+ ng’ombe, nkhosa, mbuzi,
2 “Uzani ana a Isiraeli kuti, ‘Zolengedwa zimene mungadye+ pa nyama zonse zimene zili padziko lapansi ndi izi: