Levitiko 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chimodzimodzinso kalulu,+ chifukwa amabzikula, koma ziboda zake n’zosagawanika. Akhale wodetsedwa kwa inu.
6 Chimodzimodzinso kalulu,+ chifukwa amabzikula, koma ziboda zake n’zosagawanika. Akhale wodetsedwa kwa inu.