Levitiko 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Zimene mungadye pa zonse za m’madzi ndi izi: Chilichonse cha m’madzi+ chokhala ndi zipsepse ndi mamba,+ chopezeka m’nyanja ndi m’mitsinje mungadye.
9 “‘Zimene mungadye pa zonse za m’madzi ndi izi: Chilichonse cha m’madzi+ chokhala ndi zipsepse ndi mamba,+ chopezeka m’nyanja ndi m’mitsinje mungadye.