Levitiko 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Pakati pa zolengedwa zouluka,+ izi zikhale zonyansa kwa inu. Siziyenera kudyedwa chifukwa ndi zonyansa: Chiwombankhanga,+ nkhwazi ndi muimba wakuda.
13 “‘Pakati pa zolengedwa zouluka,+ izi zikhale zonyansa kwa inu. Siziyenera kudyedwa chifukwa ndi zonyansa: Chiwombankhanga,+ nkhwazi ndi muimba wakuda.