Deuteronomo 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti aliyense wochita zimenezi, aliyense wosachita chilungamo, n’ngonyansa kwa Yehova Mulungu wako.+ Ezekieli 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ngati salandira chiwongoladzanja akabwereketsa zinthu,+ ndiponso sakongoza zinthu mwa katapira,*+ ngati sachita zopanda chilungamo,+ ngati amachita chilungamo chenicheni poweruza munthu ndi mnzake,+ Mika 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+
16 Pakuti aliyense wochita zimenezi, aliyense wosachita chilungamo, n’ngonyansa kwa Yehova Mulungu wako.+
8 ngati salandira chiwongoladzanja akabwereketsa zinthu,+ ndiponso sakongoza zinthu mwa katapira,*+ ngati sachita zopanda chilungamo,+ ngati amachita chilungamo chenicheni poweruza munthu ndi mnzake,+
8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+