Deuteronomo 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 muzifunafuna, kufufuza ndi kufunsitsa za nkhani imeneyo.+ Mukapeza kuti ndi zoonadi, choipa chimenechi chachitikadi pakati panu, Yohane 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Chilamulo chathu sichiweruza munthu asanafotokoze maganizo ake choyamba+ ndi kudziwa zochita zake, chimatero ngati?”
14 muzifunafuna, kufufuza ndi kufunsitsa za nkhani imeneyo.+ Mukapeza kuti ndi zoonadi, choipa chimenechi chachitikadi pakati panu,
51 “Chilamulo chathu sichiweruza munthu asanafotokoze maganizo ake choyamba+ ndi kudziwa zochita zake, chimatero ngati?”