Ekisodo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ana aamuna a Merari anali Mali ndi Musi.+ Amenewa ndiwo anali mabanja a Alevi malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+ Numeri 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ana a Merari,+ malinga ndi mayina a mabanja awo, anali Mali+ ndi Musi.+ Awa ndiwo anali mabanja a Alevi, potsata nyumba za makolo awo. 1 Mbiri 6:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Ana a Merari+ potsata mabanja awo anapatsidwa mizinda kuchokera ku fuko la Rubeni,+ fuko la Gadi,+ ndi fuko la Zebuloni.+ Anapatsidwa mizinda 12 atachita maere.
19 Ndipo ana aamuna a Merari anali Mali ndi Musi.+ Amenewa ndiwo anali mabanja a Alevi malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+
20 Ana a Merari,+ malinga ndi mayina a mabanja awo, anali Mali+ ndi Musi.+ Awa ndiwo anali mabanja a Alevi, potsata nyumba za makolo awo.
63 Ana a Merari+ potsata mabanja awo anapatsidwa mizinda kuchokera ku fuko la Rubeni,+ fuko la Gadi,+ ndi fuko la Zebuloni.+ Anapatsidwa mizinda 12 atachita maere.