1 Mbiri 6:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Mabanja ena a ana a Kohati anapatsidwa mizinda m’dera lawo kuchokera ku fuko la Efuraimu.+