Yoswa 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mizinda yotsatirayi ya m’gawo la Isakara ndi Aseri, pamodzi ndi anthu ake ndi midzi yake yozungulira, inali ya Manase:+ Beti-seani,+ Ibuleamu,+ Dori,+ Eni-dori,+ Taanaki,+ ndi Megido.+ Madera atatu amapiri analinso ake. Oweruza 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.Pamenepo mafumu a Kanani anamenya nkhondo,+Anamenya nkhondo ku Taanaki,+ pafupi ndi madzi a ku Megido.+Iwo sanapezepo phindu la siliva.+
11 Mizinda yotsatirayi ya m’gawo la Isakara ndi Aseri, pamodzi ndi anthu ake ndi midzi yake yozungulira, inali ya Manase:+ Beti-seani,+ Ibuleamu,+ Dori,+ Eni-dori,+ Taanaki,+ ndi Megido.+ Madera atatu amapiri analinso ake.
19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.Pamenepo mafumu a Kanani anamenya nkhondo,+Anamenya nkhondo ku Taanaki,+ pafupi ndi madzi a ku Megido.+Iwo sanapezepo phindu la siliva.+