Yoswa 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako malirewo anakhota n’kubwerera kulowera kum’mawa kwa Saridi mpaka kumalire a Kisilotu-tabori. Ndiyeno anapitirira kukafika ku Daberati+ mpaka ku Yafiya. 1 Mbiri 6:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Kuchokera ku fuko la Isakara, anawapatsa mzinda wa Kedesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Daberati+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
12 Kenako malirewo anakhota n’kubwerera kulowera kum’mawa kwa Saridi mpaka kumalire a Kisilotu-tabori. Ndiyeno anapitirira kukafika ku Daberati+ mpaka ku Yafiya.
72 Kuchokera ku fuko la Isakara, anawapatsa mzinda wa Kedesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Daberati+ ndi malo ake odyetserako ziweto,