Yoswa 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Remeti, Eni-ganimu,+ Eni-hada, ndi Beti-pazezi. 1 Mbiri 6:73 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 73 mzinda wa Ramoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Anemu+ ndi malo ake odyetserako ziweto.
73 mzinda wa Ramoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Anemu+ ndi malo ake odyetserako ziweto.