Yoswa 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuchokera kumeneko, malirewo analowera chakum’mawa n’kukafika ku Gati-heferi,+ ku Eti-kazini, ndi ku Rimoni, mpaka ku Nea. 1 Mbiri 6:77 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 77 Kuchokera ku fuko la Zebuloni,+ anapatsa ana a Merari amene anatsala, mzinda wa Rimono+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Tabori ndi malo ake odyetserako ziweto.
13 Kuchokera kumeneko, malirewo analowera chakum’mawa n’kukafika ku Gati-heferi,+ ku Eti-kazini, ndi ku Rimoni, mpaka ku Nea.
77 Kuchokera ku fuko la Zebuloni,+ anapatsa ana a Merari amene anatsala, mzinda wa Rimono+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Tabori ndi malo ake odyetserako ziweto.