Ekisodo 39:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndipo Mose ataona ntchito yonse, anaona kuti achita zonse monga mmene Yehova analamulira. Iwo anachitadi momwemo. Pamenepo Mose anawadalitsa.+ Yoswa 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Yoswa anadalitsa Kalebe mwana wa Yefune, ndi kum’patsa mzinda wa Heburoni monga cholowa chake.+ 2 Samueli 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Davide atamaliza kupereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano, anadalitsa+ anthu m’dzina la Yehova+ wa makamu.
43 Ndipo Mose ataona ntchito yonse, anaona kuti achita zonse monga mmene Yehova analamulira. Iwo anachitadi momwemo. Pamenepo Mose anawadalitsa.+
13 Pamenepo Yoswa anadalitsa Kalebe mwana wa Yefune, ndi kum’patsa mzinda wa Heburoni monga cholowa chake.+
18 Davide atamaliza kupereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano, anadalitsa+ anthu m’dzina la Yehova+ wa makamu.