Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 17:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 koma osabwera nayo pakhomo la chihema chokumanako kuti aipereke kwa Yehova,+ munthu ameneyo ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+

  • Deuteronomo 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno malo+ amene Yehova Mulungu wanu adzasankha kuti pakhale dzina lake n’kumene muzidzabweretsa zonse zimene ndikukulamulani, nsembe zanu zopsereza+ ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,+ chopereka+ chochokera m’manja mwanu ndi zonse zimene mwasankha kukhala nsembe zanu za lonjezo,+ zimene mudzalonjeza Yehova.

  • Deuteronomo 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma muzidzapereka nsembe zanu zopsereza pamalo amene Yehova adzasankhe mu limodzi la mafuko anu, ndipo muzichita zonse zimene ndakulamulani pamalo amenewo.+

  • Deuteronomo 12:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ukatero uzipereka nsembe zako zopsereza,+ nyama ndi magazi,+ paguwa lansembe la Yehova Mulungu wako. Magazi a nsembe zako uziwathira pansi pafupi ndi guwa lansembe la Yehova+ Mulungu wako, koma nyamayo utha kuidya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena