Genesis 31:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Labani anapitiriza kulankhula kuti: “Mulu wa miyalawu ndi mboni yathu lero pakati pa ine ndi iwe.” N’chifukwa chake unatchedwa Galeeda,+ Yoswa 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yoswa anauza anthu onsewo kuti: “Taonani! Mwala uwu ukhala mboni yotsutsana nafe,+ chifukwa mwalawu wamva mawu onse amene Yehova walankhula kwa ife, ndipo ukhala mboni kwa inu kuti musadzakane Mulungu wanu.”
48 Labani anapitiriza kulankhula kuti: “Mulu wa miyalawu ndi mboni yathu lero pakati pa ine ndi iwe.” N’chifukwa chake unatchedwa Galeeda,+
27 Kenako Yoswa anauza anthu onsewo kuti: “Taonani! Mwala uwu ukhala mboni yotsutsana nafe,+ chifukwa mwalawu wamva mawu onse amene Yehova walankhula kwa ife, ndipo ukhala mboni kwa inu kuti musadzakane Mulungu wanu.”