Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mudzathamangitsa adani anu+ ndi kuwagonjetsa ndi lupanga.

  • Deuteronomo 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Koma khalani tcheru ndipo musamale moyo wanu,+ kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona,+ ndi kuti mitima yanu isaiwale zinthu zimenezo masiku onse a moyo wanu.+ Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauza za zinthu zimenezo,+

  • Yoswa 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atafika pamalo otsetsereka otchedwa Beti-horoni pothawa Aisiraeli, Yehova anawagwetsera miyala ikuluikulu ya matalala+ kuchokera kumwamba yomwe inawagwera ndi kuwapha mpaka kukafika ku Azeka. Amene anaphedwa ndi matalalawo anali ambiri kuposa amene ana a Isiraeli anapha ndi lupanga.

  • Yoswa 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho dzuwa linaimadi, ndiponso mwezi unaima mpaka mtunduwo utalanga adani ake.+ Kodi sizinalembedwe m’buku la Yasari?+ Dzuwa linaima kumwamba pakatikati, silinafulumire kulowa pafupifupi kwa tsiku lonse lathunthu.+

  • Yoswa 10:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Choncho Yoswa anapha anthu a m’dera lonse la mapiri,+ anthu a ku Negebu,+ a ku Sefela,+ ndi a m’madera otsetsereka+ pamodzi ndi mafumu awo onse. Iye anaonetsetsa kuti pasakhale wopulumuka,+ ndipo anapha chamoyo chilichonse*+ monga mmene Yehova Mulungu wa Isiraeli analamulira.+

  • Yoswa 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Analandanso dera lochokera kuphiri la Halaki+ lomwe lili moyang’anizana ndi Seiri+ mpaka kukafika ku Baala-gadi,+ kuchigwa cha Lebanoni m’munsi mwa phiri la Herimoni.+ Yoswa anagwira mafumu awo onse ndi kuwapha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena