Ekisodo 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ndimasonyeza kukoma mtima kosatha ku mibadwo masauzande chifukwa cha anthu amene amandikonda ndi kusunga malamulo anga.+ Deuteronomo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse,+ moyo wako wonse,+ ndi mphamvu zako zonse.+ Mateyu 22:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iye anamuyankha kuti: “‘Uzikonda Yehova* Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, ndi maganizo ako onse.’+ 1 Akorinto 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ngati munthu akukonda Mulungu,+ ameneyo amadziwika kwa Mulungu.+
6 Koma ndimasonyeza kukoma mtima kosatha ku mibadwo masauzande chifukwa cha anthu amene amandikonda ndi kusunga malamulo anga.+
37 Iye anamuyankha kuti: “‘Uzikonda Yehova* Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, ndi maganizo ako onse.’+