Oweruza 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho nanenso ndikuti, ‘Sindiwapitikitsa pamaso panu, koma akhala msampha kwa inu,+ ndipo milungu yawo ikhala ngati nyambo.’”+ Oweruza 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ine sindipitikitsanso pamaso pawo mtundu uliwonse pa mitundu imene Yoswa anaisiya pamene ankamwalira.+ Oweruza 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Aisiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Kusani-risataimu, mfumu ya Mesopotamiya.+ Ana a Isiraeli anatumikira Kusani-risataimu zaka 8.
3 Choncho nanenso ndikuti, ‘Sindiwapitikitsa pamaso panu, koma akhala msampha kwa inu,+ ndipo milungu yawo ikhala ngati nyambo.’”+
21 ine sindipitikitsanso pamaso pawo mtundu uliwonse pa mitundu imene Yoswa anaisiya pamene ankamwalira.+
8 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Aisiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Kusani-risataimu, mfumu ya Mesopotamiya.+ Ana a Isiraeli anatumikira Kusani-risataimu zaka 8.