Genesis 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Abulahamu anatcha mwana amene Sara anamuberekerayo dzina lakuti Isaki.+ Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+