Nehemiya 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Pamenepo munawapatsa maufumu+ ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo chigawo ndi chigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ dziko la mfumu ya Hesiboni+ ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.+ Salimo 135:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+
22 “Pamenepo munawapatsa maufumu+ ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo chigawo ndi chigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ dziko la mfumu ya Hesiboni+ ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.+
11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+