Yoswa 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ansembe onyamula likasa la pangano la Yehova anangoima chilili panthaka youma+ pakati pa mtsinje wa Yorodano. Anaimabe choncho pamene Aisiraeli onse anali kuwoloka panthaka youmayo,+ kufikira mtundu wonse unatha kuwoloka mtsinje wa Yorodano. Salimo 114:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyanja inaona ndipo inathawa.+Yorodano anabwerera m’mbuyo.+
17 Ansembe onyamula likasa la pangano la Yehova anangoima chilili panthaka youma+ pakati pa mtsinje wa Yorodano. Anaimabe choncho pamene Aisiraeli onse anali kuwoloka panthaka youmayo,+ kufikira mtundu wonse unatha kuwoloka mtsinje wa Yorodano.