Genesis 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano Abulamu anayenda m’dzikomo mpaka kukafika ku Sekemu,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya More.+ Pa nthawiyo n’kuti m’dzikomo muli Akanani. Genesis 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho anthuwo anapereka kwa Yakobo milungu yachilendo+ yonse imene anali nayo, ndi ndolo* zimene anavala m’makutu. Kenako Yakobo anafotsera+ zinthuzo pansi pa mtengo waukulu pafupi ndi Sekemu.
6 Tsopano Abulamu anayenda m’dzikomo mpaka kukafika ku Sekemu,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya More.+ Pa nthawiyo n’kuti m’dzikomo muli Akanani.
4 Choncho anthuwo anapereka kwa Yakobo milungu yachilendo+ yonse imene anali nayo, ndi ndolo* zimene anavala m’makutu. Kenako Yakobo anafotsera+ zinthuzo pansi pa mtengo waukulu pafupi ndi Sekemu.