Deuteronomo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inuyo mukudziwa bwino lero, (sindikulankhulatu ndi ana anu amene sanadziwe ndi kuona chilango* cha Yehova+ Mulungu wanu, ukulu wake+ ndi dzanja lake lamphamvu+ ndi mkono wake wotambasula,+ Deuteronomo 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana awo amene sadziwa chilamulo ichi azimvetsera,+ ndipo aphunzire kuopa Yehova Mulungu wanu masiku onse amene mudzakhala panthaka imene mukupita kukaitenga kukhala yanu,+ mutawoloka Yorodano.”
2 Inuyo mukudziwa bwino lero, (sindikulankhulatu ndi ana anu amene sanadziwe ndi kuona chilango* cha Yehova+ Mulungu wanu, ukulu wake+ ndi dzanja lake lamphamvu+ ndi mkono wake wotambasula,+
13 Ana awo amene sadziwa chilamulo ichi azimvetsera,+ ndipo aphunzire kuopa Yehova Mulungu wanu masiku onse amene mudzakhala panthaka imene mukupita kukaitenga kukhala yanu,+ mutawoloka Yorodano.”