Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 sadzaliona m’pang’ono pomwe dziko limene ndinalumbirira makolo awo. Ndithudi, onse amene sakundipatsa ulemu, sadzaliona dzikolo.+

  • Deuteronomo 1:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 ‘Palibe munthu ndi mmodzi yemwe mwa anthu a m’badwo woipa uwu amene adzaona dziko labwino limene ndinalumbira kuti ndidzalipereka kwa makolo anu,+

  • Salimo 106:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Choncho Mulungu anawalumbirira atakweza dzanja lake,+

      Kuti adzawapha m’chipululu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena