Ekisodo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’mwezi woyamba, tsiku la 14 la mwezi umenewo, madzulo muzidzadya mikate yopanda chofufumitsa, mpaka kukafika madzulo a tsiku la 21 mwezi womwewo.+ Ekisodo 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Muzidzadya mikate yosafufumitsa masiku 7,+ ndipo pa tsiku la 7 limenelo muzidzachita chikondwerero kwa Yehova.+ Levitiko 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Pa tsiku la 15 m’mwezi umenewu, muzichita chikondwerero cha Yehova cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa imeneyi masiku 7.+
18 M’mwezi woyamba, tsiku la 14 la mwezi umenewo, madzulo muzidzadya mikate yopanda chofufumitsa, mpaka kukafika madzulo a tsiku la 21 mwezi womwewo.+
6 Muzidzadya mikate yosafufumitsa masiku 7,+ ndipo pa tsiku la 7 limenelo muzidzachita chikondwerero kwa Yehova.+
6 “‘Pa tsiku la 15 m’mwezi umenewu, muzichita chikondwerero cha Yehova cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa imeneyi masiku 7.+