Deuteronomo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tamverani Aisiraeli inu, lero mukuwoloka Yorodano+ kulowa m’dziko limene mukukalilanda kwa mitundu ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa inuyo.+ Mukukalanda mizinda ikuluikulu yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+ Deuteronomo 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti mukuwoloka Yorodano ndi kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala lanu. Mukalitengedi ndi kukhala momwemo.+ Yoswa 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Patatha masiku atatu aja,+ akapitawo+ a anthuwo anapita mumsasa,
9 “Tamverani Aisiraeli inu, lero mukuwoloka Yorodano+ kulowa m’dziko limene mukukalilanda kwa mitundu ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa inuyo.+ Mukukalanda mizinda ikuluikulu yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+
31 Pakuti mukuwoloka Yorodano ndi kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala lanu. Mukalitengedi ndi kukhala momwemo.+