Yoswa 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo anauza Yoswa kuti: “Yehova wapereka dziko lonselo m’manja mwathu.+ Ndipo anthu onse a m’dzikomo akuchita mantha chifukwa cha ife.”+ Salimo 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munakondwera nawo.+ Machitidwe 7:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndipo makolo athu amene anachilandira kwa makolo awo, analowa nacho limodzi ndi Yoswa,+ m’dziko limene linali m’manja mwa anthu a mitundu ina+ amene Mulungu anawapitikitsa pamaso pa makolo athu.+ Chihemacho chinakhala m’dziko limeneli mpaka m’masiku a Davide.
24 Iwo anauza Yoswa kuti: “Yehova wapereka dziko lonselo m’manja mwathu.+ Ndipo anthu onse a m’dzikomo akuchita mantha chifukwa cha ife.”+
3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munakondwera nawo.+
45 Ndipo makolo athu amene anachilandira kwa makolo awo, analowa nacho limodzi ndi Yoswa,+ m’dziko limene linali m’manja mwa anthu a mitundu ina+ amene Mulungu anawapitikitsa pamaso pa makolo athu.+ Chihemacho chinakhala m’dziko limeneli mpaka m’masiku a Davide.