Yoswa 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo amuna a ku Aiwo anapha amuna achiisiraeli pafupifupi 36. Anawathamangitsabe+ kuchokera kuchipata mpaka ku Sebarimu, n’kupitiriza kuwapha mpaka pamalo otsetsereka. Zitatero, mitima ya Aisiraeli onse inasungunuka ndi mantha.+
5 Ndipo amuna a ku Aiwo anapha amuna achiisiraeli pafupifupi 36. Anawathamangitsabe+ kuchokera kuchipata mpaka ku Sebarimu, n’kupitiriza kuwapha mpaka pamalo otsetsereka. Zitatero, mitima ya Aisiraeli onse inasungunuka ndi mantha.+