Oweruza 20:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ana a Benjamini ataona kuti amuna a Isiraeli akuthawa,+ anaganiza kuti akugonja. Koma iwo anali kuthawa chifukwa anali kudalira amuna amene anawaika kuti abisalire mzinda wa Gibeya.
36 Ana a Benjamini ataona kuti amuna a Isiraeli akuthawa,+ anaganiza kuti akugonja. Koma iwo anali kuthawa chifukwa anali kudalira amuna amene anawaika kuti abisalire mzinda wa Gibeya.