Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 32:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Pamenepo Mose anagawira malo ana a Gadi+ ndi ana a Rubeni.+ Anagawiranso malo hafu ya fuko la Manase+ mwana wa Yosefe. Anawagawira malo a ufumu wa Sihoni+ mfumu ya Aamori, ndi a ufumu wa Ogi+ mfumu ya Basana, dera lonse la mizinda ndi midzi yozungulira.

  • Yoswa 22:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Zitatero, ana a Rubeni, ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase, anachoka ku Silo kumene kunali ana ena a Isiraeli m’dziko la Kanani. Anapita ku Giliyadi,+ dziko lawo limene anapatsidwa ndi Mose molamulidwa ndi Yehova, ndiponso limene anakhazikikamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena