Levitiko 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Mukapitiriza kutsatira malangizo anga ndi kusunga malamulo anga,+ Deuteronomo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Madalitso onsewa adzakutsata ndi kukupeza+ chifukwa ukumvera mawu a Yehova Mulungu wako: