Deuteronomo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musawonjezepo kalikonse pa mawu amene ndikukulamulani, ndipo musachotsepo kalikonse pa mawu amenewa,+ kuti musunge malamulo a Yehova Mulungu wanu amene ndikukupatsani. Deuteronomo 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Muzichita mosamala mawu onse amene ndikukuuzani.+ Musawonjezepo kapena kuchotsapo kalikonse.+
2 Musawonjezepo kalikonse pa mawu amene ndikukulamulani, ndipo musachotsepo kalikonse pa mawu amenewa,+ kuti musunge malamulo a Yehova Mulungu wanu amene ndikukupatsani.