Numeri 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Um’patseko ulemerero wako,+ kuti khamu lonse la ana a Isiraeli lizimumvera.+ Deuteronomo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yoswa mwana wa Nuni anali wodzazidwa ndi mzimu wa nzeru,+ pakuti Mose anaika manja ake pa iye.+ Choncho ana a Isiraeli anayamba kumumvera ndipo iwo anayamba kuchita monga momwe Yehova analamulira Mose.+
9 Yoswa mwana wa Nuni anali wodzazidwa ndi mzimu wa nzeru,+ pakuti Mose anaika manja ake pa iye.+ Choncho ana a Isiraeli anayamba kumumvera ndipo iwo anayamba kuchita monga momwe Yehova analamulira Mose.+