22 Ndiponso, palibe munthu amene amathira vinyo watsopano m’matumba achikopa akale. Akachita zimenezo, vinyoyo amaphulitsa matumbawo. Kenako vinyoyo amatayika ndipo matumbawo amawonongeka.+ Koma anthu amathira vinyo watsopano m’matumba achikopa atsopano.”+