Ekisodo 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Usatemberere Mulungu+ kapena kutemberera mtsogoleri amene ali pakati pa anthu ako.+ Afilipi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muzichita zinthu zonse popanda kung’ung’udza+ ndi kutsutsana,+