Levitiko 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu aliyense woperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+ Yoswa 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aliyense amene anali mumzindawo anamupha ndi lupanga, kuyambira amuna, akazi, anyamata ndi nkhalamba zomwe. Anaphanso ng’ombe, nkhosa, ndi abulu.+
29 Munthu aliyense woperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+
21 Aliyense amene anali mumzindawo anamupha ndi lupanga, kuyambira amuna, akazi, anyamata ndi nkhalamba zomwe. Anaphanso ng’ombe, nkhosa, ndi abulu.+