Salimo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sindidzaopa anthu masauzande makumimakumiAmene andiukira ndi kundizungulira.+ Salimo 118:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mitundu yonse ya anthu inandizungulira,+Koma ndinali kuikankhira kutali m’dzina la Yehova.+