Numeri 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+
2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+