Ekisodo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+ Levitiko 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Choncho mudzipatule monga anthu oyera,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.
10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+