Yoswa 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+
17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+