Oweruza 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atapereka Heburoni kwa Kalebe monga mmene Mose analonjezera,+ Kalebe anapitikitsa ana atatu aamuna a Anaki amene anali kukhala mmenemo.+
20 Atapereka Heburoni kwa Kalebe monga mmene Mose analonjezera,+ Kalebe anapitikitsa ana atatu aamuna a Anaki amene anali kukhala mmenemo.+