Oweruza 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo iye anati: “Ndidalitseni,+ pakuti mwandipatsa malo akum’mwera, ndipo mundipatse Guloti-maimu.”* Pamenepo Kalebe anam’patsa Guloti Wakumtunda+ ndi Guloti Wakumunsi.
15 Ndipo iye anati: “Ndidalitseni,+ pakuti mwandipatsa malo akum’mwera, ndipo mundipatse Guloti-maimu.”* Pamenepo Kalebe anam’patsa Guloti Wakumtunda+ ndi Guloti Wakumunsi.