Numeri 14:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Koma Aamaleki+ ndi Akanani omwe anali kukhala kudera lamapirilo anatsika n’kuyamba kuwapha ndi kuwabalalitsa mpaka ku Horima.+ Deuteronomo 1:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Kumeneko Aamori okhala m’phiri limenelo anatuluka kudzakumana nanu ndipo anakuthamangitsani,+ mmene njuchi zimachitira, ndi kukubalalitsani m’phiri la Seiri mpaka kukafika ku Horima.+ Yoswa 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Elitoladi,+ Betuli, Horima, Oweruza 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma a fuko la Yuda anayendabe ndi abale awo a fuko la Simiyoni, ndipo anapha Akanani okhala ku Zefati ndi kuwononga mzindawo.+ N’chifukwa chake mzindawo unatchedwa Horima.*+
45 Koma Aamaleki+ ndi Akanani omwe anali kukhala kudera lamapirilo anatsika n’kuyamba kuwapha ndi kuwabalalitsa mpaka ku Horima.+
44 Kumeneko Aamori okhala m’phiri limenelo anatuluka kudzakumana nanu ndipo anakuthamangitsani,+ mmene njuchi zimachitira, ndi kukubalalitsani m’phiri la Seiri mpaka kukafika ku Horima.+
17 Koma a fuko la Yuda anayendabe ndi abale awo a fuko la Simiyoni, ndipo anapha Akanani okhala ku Zefati ndi kuwononga mzindawo.+ N’chifukwa chake mzindawo unatchedwa Horima.*+