Yoswa 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu aliyense wopandukira malamulo anu,+ ndi wosamvera mawu anu pa chilichonse chimene mungamulamule, ameneyo aphedwe.+ Inuyo mukhale wolimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.”+
18 Munthu aliyense wopandukira malamulo anu,+ ndi wosamvera mawu anu pa chilichonse chimene mungamulamule, ameneyo aphedwe.+ Inuyo mukhale wolimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.”+