Numeri 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo anakaimirira pamaso pa Mose, pamaso pa wansembe Eleazara,+ pamaso pa atsogoleri ndi khamu lonse, pakhomo la chihema chokumanako, n’kunena kuti: Numeri 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Amuna amene akakugawireni malo monga cholowa chanu, mayina awo ndi awa: Wansembe Eleazara+ ndi Yoswa mwana wa Nuni.+ Yoswa 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Limeneli ndilo dziko limene ana a Isiraeli anatenga monga cholowa chawo m’dziko la Kanani.+ Wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mafuko a makolo a ana a Isiraeli, ndiwo anagawa dzikolo kuti likhale cholowa chawo.+
2 Iwo anakaimirira pamaso pa Mose, pamaso pa wansembe Eleazara,+ pamaso pa atsogoleri ndi khamu lonse, pakhomo la chihema chokumanako, n’kunena kuti:
17 “Amuna amene akakugawireni malo monga cholowa chanu, mayina awo ndi awa: Wansembe Eleazara+ ndi Yoswa mwana wa Nuni.+
14 Limeneli ndilo dziko limene ana a Isiraeli anatenga monga cholowa chawo m’dziko la Kanani.+ Wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mafuko a makolo a ana a Isiraeli, ndiwo anagawa dzikolo kuti likhale cholowa chawo.+