Numeri 33:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Mukalande dzikolo n’kukhalamo, chifukwa ndidzalipereka ndithu kwa inu kuti likhale lanu.+ Deuteronomo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mizinda yokhayi ya anthu awa a mitundu ina imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, ndi imene simuyenera kusiyamo chilichonse chopuma chili chamoyo,+
16 Mizinda yokhayi ya anthu awa a mitundu ina imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, ndi imene simuyenera kusiyamo chilichonse chopuma chili chamoyo,+