Deuteronomo 4:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 ndipo anamulanda dziko lakelo ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana. Amenewa ndi mafumu awiri a Aamori amene anali kuchigawo chotulukira dzuwa cha Yorodano.
47 ndipo anamulanda dziko lakelo ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana. Amenewa ndi mafumu awiri a Aamori amene anali kuchigawo chotulukira dzuwa cha Yorodano.