Numeri 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+ Numeri 26:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Amenewa ndiwo amuna onse amene anawerengedwa pakati pa ana a Isiraeli. Onse pamodzi analipo 601,730.+ Numeri 26:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Zinakhala choncho chifukwa ponena za iwo, Yehova anati: “Mulimonsemo adzafera m’chipululu basi.”+ Choncho, sipanatsale ndi mmodzi yemwe kupatulapo Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+
29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+
51 Amenewa ndiwo amuna onse amene anawerengedwa pakati pa ana a Isiraeli. Onse pamodzi analipo 601,730.+
65 Zinakhala choncho chifukwa ponena za iwo, Yehova anati: “Mulimonsemo adzafera m’chipululu basi.”+ Choncho, sipanatsale ndi mmodzi yemwe kupatulapo Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+