Oweruza 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pa Yefita, Ibizani wa ku Betelehemu+ anayamba kuweruza Isiraeli.+